×
Image

QUR’AN YOLEMEKEZEKA yotanthauzidwa m’Chichewa ndi - (Chichewa)

QUR’AN YOLEMEKEZEKA yotanthauzidwa m’Chichewa ndi

Image

QUR’AN YOLEMEKEZEKA yotanthauzidwa m’chichewa - (Chichewa)

Chifukwa chakufunika kwa uthengawu kuti ufike kwa anthu onse, a Bungwe la Africa Muslim Agency adandipempha kuti ndimasulire Qur’an m’chichewa, ndicholinga chakuti amene sangathe kumvetsa uthenga wake m’chiarabu, aumve m’chilankhulo chawo cha Chichewa. Choncho ntchitoyi idagwirikadi kotero kuti munthu akawerenga bwinobwino akhoza kumva uthenga wa Mulungu m’Qur’an. Ndayetsetsa m’kutanthauzira kwanga....

Image

TANTHAWUZO LACHISILAMU M’CHICHEWA - (Chichewa)

-

Image

IslamHouse.com - (Chichewa)

Islamhouse is the biggest website for Islamic dawah in world languages. It contains free items in more than 100 languages, items like: books, audios,videos, posters, Islamic apps and others. https://islamhouse.com/ny/main

Image

KUSIYANA KWA AMAYI A CHISILAMU NDI AMAYI A MU CHIKHALIDWE CHA CHIYUDA NDI CHIKHRISTU - (Chichewa)

Buku ili lasonkhanitsa kakhalidwe kwa amayi m’zipembedzo zitatu: Chiyuda, Chikristu ndi Chisilamu. Bukuli lalongosola mfundo zofunikira zochokera mu Chiyuda, komwe mzimayi sanangomutchula kuti ndi wochimwa, koma anatinso ndiyemwe anamuchimwitsa mwamuna. Koma Qur’an ili ndi kuwona kosiyana ndi mabuku ena onse, poti imamuona mzimai kuti ndi wofunikira kwambiri pa chitukuko cha....

Image

CHUMA CHOBISIKA M’BAIBULO - (Chichewa)

Cholinga cha bukhuli ndi kuwaunikira anthu omwe amafuna kudziwa zoona zokhazokha, pa zauthenga weniweni womwe Yesu (mtendere ukhale pa iye) ankaphunzitsa. Bukhuli likukamba za machitidwe ena omwe analetsedwa kapena kuvomerezedwa m’Baibulo. Pali chikhulupiliro chakuti anthu akawerenga bukhuli adzipezera okha gulu lenileni la anthu lomwe limatsatira chiphunzitso cha Yesu (mtendere ukhale....